Ubatizo wa ana ang’onoang’ono ndi chonyansa choipa—Ana ang’onoang’ono ali ndi moyo mwa Khristu chifukwa cha Chitetezero—Chikhulupiliro, kulapa, kufatsa ndi kudzichepetsa kwa mtima, kulandira Mzimu Woyera, ndi kupilira mpaka ku mapeto kumatsogolera ku chipulumutso. M’dzaka za pafupifupi 401–421 Yesu Atabadwa.