Oweruza achinyengo afuna kusonkhezera anthu kutsutsana ndi Nefi—Abrahamu, Mose, Zenosi, Zenoki, Eziya, Yesaya, Yeremiya, Lehi, ndi Nefi onse adachitira umboni za Khristu—Mwa kutsogozedwa kwakudzodzedwa Nefi alengeza kuphedwa kwa oweruza wamkulu. M’dzaka za pafupifupi 23–21 Yesu Asadabadwe.